Zowonera Banja Lonse

Mpukutu wa Uthenga Wabwino

Uthenga wabwino wa Mateyu unali uthenga wabwino mu dzaka zoyambilira za Chikhirisitu. Uthenga opita kwa a Khirisitu pakupatulika kwawo kuchoka kwa Ayuda. Uthenga wabwino wa Mateyu umapita kutali kwambiri powonesela kuti, ngati Mpulumutsi, Yesu ndi kukwanilisidwa kwa ma ulosi a Chipangano Chakale ngati mpulumusi. Yojambulidwa ndi Lumo Project.