Zowonera Banja Lonse

Kusinthidwa koyamba kwa liwu ndi liwu kwa Mauthenga Abwino pogwiritsa ntchito nkhani yoyambirira monga momwe analembera - kuphatikizapo Mauthenga Abwino a Mateyu, Marko, Luka, ndi Yohane - kumatithandiza kumvetsetsa limodzi mwa malemba opatulika kwambiri a mbiri yakale.

Magawo

 • Uthenga wabwino wa Mateyu (3h 9m)

  Uthenga wabwino wa Mateyu unali uthenga wabwino mu dzaka zoyambilira za Chikhirisitu. Uthenga opita kwa a Khirisitu pakupatulika kwawo kuchoka kwa Ayu... more

 • Uthenga wabwino wa Maliko (2h 3m)

  Uthenga Wabwino wa Maliko ojambulidwa ndi The Lumo Project ukubweretsa kufotokozera kwenikweni pogwiritsa ntchito Uthenga wabwino, liwu kwa liwu.

 • Uthenga wabino was Luka (3h 24m)

  UTHENGA WABWINO WA LUKA, kuposa wina uliwonse, umagwirizana ndi mbiri yakale. Luka, monga “wofotokozera” zochitika, amawona Yesu kukhala “Mpulumutsi” ... more

 • Uthenga wabwino wa Yohane (2h 40m)

  UTHENGA WABWINO WA YOHANE ndi buku loyamba kujambulidwa la Baibulo monga momwe linalembedwera. Kugwiritsa ntchito nkhani yoyambirira ya Yesu monga kal... more